Zii
[00:00.13] Mic check ²
[00:03.05] 1, 2,1, 2
[00:05.17] Ase wayamba ku recorder
[00:07.17] (Oky tiyen tiyambe)
[00:10.89] Mtima ukapuma
[00:19.11] Zichewa pakamwa
[00:24.85] Mudzi nawo umasungulumwa
[00:29.64] Tinali naye zulo
[00:32.56] Tadya naye nkhomalilo
[00:34.69] Ohh ndatopa masomu tulo
[00:37.35] Tiwonana mawa ndikaone pillow
[00:40.45] Sindikuziwa chizanditenge ndichani
[00:43.19] Chonde musazalile inu
[00:45.31] Mzimu wanga uzazazidwa ndichimwemwe
[00:47.97] Musazadandaule
[00:50.57] Auzeni alowe
[00:52.77] Andione nkhope komaliza
[00:55.58] Akamaliza andipelekeze
[00:57.82] Malo a ziwoo
[01:00.48] Auzeni alowe andione nkophe komaliza andipelekeze
[01:07.37] Malo a Zii wo
[01:10.86] Aaa ndizakhala pompo ndili mu form ya mzimu
[01:13.78] Ndizizaona chilichonse
[01:16.42] Osaopa sindizaona zinazo
[01:19.62] Timiseche sindizamva nawo
[01:22.01] Adzukulu azakusana makasu mammawa mwina
[01:26.79] Azimayi masana azaimba hosannah
[01:31.33] Malo azii timukonzele mudzi
[01:35.03] Anyamata tikumbe pati
[01:37.99] Apoo ayi pali miyala
[01:40.11] Apa bwino pali a ujee
[01:42.23] Akapume akatchole batcha ndi mbalame
[01:45.97] Kanali ka nyamata kokonda nthabwala
[01:48.88] Auzeni anambe kumphikako njala(aaa ntchito timadyela)
[01:51.54] Ndye ndizizangoseka
[01:54.72] Malo aziiwo
[01:56.59] Mu nzimu ndizasuzumila kumphika
[01:58.97] Malo aziiwo
[02:01.63] Anambe akusinkha ndiwo
[02:05.23] Malo aziiwo
[02:06.45] Ena mwa mwayi azapeza banja
[02:09.89] Malo aziiwo
[02:12.02] Malo aziiwo
[02:15.21] Malo aziiwo
[02:18.15] Malo aziiwo
[02:20.01] Malo aziiwo
[02:22.40] Malo aziiwo
[02:25.32] Malo aziiwo
[02:27.70] Malo aziiwo
[02:33.29] Ndizamva wizulo amayi amvano
[02:37.28] Oohh kani ndikakondedwa chonchi
[02:41.26] Malawilano!!
[02:43.91] Mayambililo tapanga chimvano
[02:45.78] Mukamazalila ndizasisima
[02:48.69] Zalitonthozeni kholo langa,
[02:51.08] Azibale anga, azinzanga!!
