Lrc Player

Zapadziko

Stonard Lungu ft. San B
[07:06.95]·
This lyric sheet isn't paired with a song yet, so lines are shown but won't sync or seek.

[00:25.74] - Zapadziko inu

[00:27.87] - Zapadziko

[00:29.19] - Zapadziko

[00:31.05] - Anzanga nzachabe'chabe

[00:33.17] - Mbadwo wina nubadwa ena nupita

[00:37.16] - Kutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[00:42.20] - Gwada pansi

[00:51.52] - Nupempere

[00:52.84] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[00:57.10] - Amapatsa

[00:58.96] - Ndipo amalanda

[01:01.08] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[01:05.60] - Gwada pansi

[01:08.25] - Nupempere

[01:10.38] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[01:13.83] - Amapatsa

[01:15.97] - Ndipo amalanda

[01:18.64] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[01:39.38] - Tawonani malemba

[01:41.77] - Akwanilitsidwa

[01:43.63] - Kuti dziko lapansi, anzanga, ndi nkhondozokha

[01:47.88] - Kodi anzanga inu

[01:50.53] - Zapadziko

[01:52.39] - Mutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[01:56.64] - Tawonani malemba

[01:59.30] - Akwanilitsidwa

[02:00.90] - Kuti dziko lapansi, anzanga, ndi nkhondozokha

[02:05.15] - Kodi anzanga inu

[02:07.27] - Zapadziko

[02:09.42] - Mutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[02:13.67] - Gwada pansi

[02:15.80] - Nupempere

[02:17.93] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[02:21.91] - Amapatsa

[02:24.04] - Ndipo amalanda

[02:26.42] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[02:30.41] - Gwada pansi

[02:32.80] - Nupempere

[02:35.19] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[02:39.17] - Amapatsa

[02:40.77] - Ndipo amalanda

[02:43.18] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[03:38.44] - Zapadziko inu

[03:48.80] - Zapadziko

[03:50.67] - Zapadziko

[03:52.52] - Anzanga nzachabe'chabe

[03:54.91] - Mbadwo wina nubadwa ena nupita

[03:58.90] - Kutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[04:12.17] - Zapadziko inu

[04:14.31] - Zapadziko

[04:16.96] - Zapadziko

[04:18.29] - Anzanga nzachabe'chabe

[04:20.94] - Mbadwo wina nubadwa ena nupita

[04:24.39] - Kutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[04:29.46] - Gwada pansi

[04:31.05] - Nupempere

[04:32.91] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[04:37.16] - Amapatsa

[04:39.81] - Ndipo amalanda

[04:41.69] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[04:46.19] - Gwada pansi

[04:48.31] - Nupempere

[04:50.18] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[04:52.03] - Amapatsa

[04:54.96] - Ndipo amalanda

[04:59.47] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[05:19.39] - Tawonani malemba

[05:21.78] - Akwanilitsidwa

[05:23.64] - Kuti dziko lapansi, anzanga, ndi nkhondozokha

[05:27.89] - Kodi anzanga inu

[05:30.55] - Zapadziko

[05:32.70] - Mutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[05:36.94] - Tawonani malemba

[05:39.33] - Akwanilitsidwa

[05:41.19] - Kuti dziko lapansi, anzanga, ndi nkhondozokha

[05:44.91] - Kodi anzanga inu

[05:47.56] - Zapadziko

[05:49.42] - Mutanji nthawi anzanga nzachabe'chabe

[05:53.94] - Gwada pansi

[05:55.53] - Nupempere

[05:57.92] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[06:01.91] - Amapatsa

[06:04.04] - Ndipo amalanda

[06:06.42] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe

[06:10.94] - Gwada pansi

[06:13.06] - Nupempere

[06:14.92] - Chomwe usowa chauta samana ayi

[06:19.18] - Amapatsa

[06:21.03] - Ndipo amalanda

[06:23.43] - Zapadziko anzanga nzachabe'chabe