Amtenga
[00:17.39] Man wo nda bhobho
[00:20.58] Si andewu ngati achina thompo
[00:22.98] Amatchilaso mwa bhobho
[00:25.37] komano mkaziyoo
[00:28.02] Mkaziyo ndi wangwilo
[00:29.61] Amafunika superhero
[00:32.32] komano man wo akumabwera ndi yawo yawo
[00:35.55] HOOK
[00:35.86] Komano amtenga aah
[00:37.98] Inuyo mupenga aa
[00:40.38] Komano antenga aah
[00:42.76] Inuyo mupeeee (nga)
[00:44.89] Komano amtenga
[00:47.00] Winayo watenga
[00:49.40] Inuyo mupenga
[00:51.79] Winayo wa nteee ee (nga)
[00:53.38] VERSE 1
[00:54.19] Mkaziyo ndi wa bhobho
[00:56.05] komano man wooo
[00:58.45] Alibe khalidwe
[01:00.57] Mkazi amangomenya
[01:02.97] Daily kugona ndi nkhawa
[01:05.36] Kenako mudanda akathawa
[01:07.76] Koma pena pake kumavomeleza
[01:10.44] Onani bondo mwa nong'oneza
[01:12.56] yeeah
[01:13.08] lalalalalalala amutenga ena
[01:17.33] lalalalalalalala amutenga ena
[01:19.72] PRE HOOK
[01:21.85] Man wo nda bhobho
[01:24.51] Si andewu ngati achina thompo
[01:27.17] Amatchilaso mwa bhobho
[01:29.29] komano mkaziyoo
[01:31.69] Mkaziyo ndi wangwilo
[01:33.80] Amafunika superhero
[01:36.20] komano man wo akumabwera ndi yawo yawo
[01:39.65] HOOK
[01:39.91] Komano amtenga aah
[01:41.78] Inuyo mupenga aa
[01:44.18] Komano antenga aah
[01:46.57] Inuyo mupeeee (nga)
[01:48.96] VERSE 2
[01:49.22] Iii inu ma man
[02:01.18] Iii inu tamvani
[02:03.83] Iii inu pali nkhani
[02:05.72] kwavuta Kumutsiku
[02:08.10] Akuchita kungananana
[02:10.23] Malaya kukwenyanana
[02:12.89] Koma amavanana (nana)
[02:16.63] iyeeeeeh
[02:17.68] Kulipo kuona ngati amakukonda
[02:19.53] Komano utazisandusa wekha mlonda
[02:21.93] Care for your partner suzapitaso kwa wina aah
[02:25.40] PRE HOOK
[02:26.23] Man wo nda bhobho
[02:28.63] Si andewu ngati achina thompo
[02:30.75] Amatchilaso mwa bhobho
[02:33.41] komano mkaziyoo
[02:35.80] Mkaziyo ndi wangwilo
[02:37.66] Amafunika superhero
[02:40.05] komano man wo akumabwera ndi yawo yawo
[02:43.51] HOOK
[02:44.04] Komano amtenga aah
[02:45.89] Inuyo mupenga aa
[02:48.30] Komano antenga aah
[02:50.41] Inuyo mupeeee (nga)
[02:52.83] OUTRO
[02:53.10] Care for your partner
[03:05.58] Care for your partner
[03:07.71] Care for your partner aaaah
[03:12.25] ayye Maone Awosh
