Kusangalala Zeze Kingston x Leumas -Zeze Kingston_ www.JustMalawi-com
[00:30.94] Eyoh tiyeni
[00:34.39] Tiyeni tiyeni tiyeni eish
[00:39.17] Una-na-na
[00:41.56] Una-na-na mmh
[00:47.15] Una-na-na
[00:49.81] Una-na-na mmh
[00:55.66] Pomwe ena akulira ena akuseka mmh
[01:04.25] Pomwe ena akulira ena akusekelera
[01:11.72] Koma masiku ako osekelera sangakhale onse dziwa
[01:20.23] Ndati masiku ako ovutika sangakhale onse dziwa
[01:29.04] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[01:32.56] Koma ine ndasankha kusangalala
[01:37.90] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[01:40.86] Koma ine ndasankha kusangalala
[01:46.46] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[01:49.39] Koma ine ndasankha kusangalala
[01:55.01] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[01:58.20] Koma ine ndasankha kusangalala
[02:45.40] Olo ndidzilira! ndilira mpaka liti?
[02:53.65] Ndidzidandaula! ndidandaula mpaka liti?
[03:02.43] Olo ndidzilira! Ndilira mpaka liti? (ndilira mpaka liti)
[03:10.68] Olo ndidzidandaula! mmh mpaka liti (ndidandaula mpaka liti)
[03:19.48] Poti mavuto samatha, mavuto samatha
[03:24.56] Mavuto samatha, mavuto samatha
[03:28.84] Mavuto samatha, mavuto samatha
[03:33.08] Mavuto samatha, mavuto samatha
[03:37.86] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[03:41.06] Koma ine ndasankha kusangalala
[03:46.36] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[03:49.58] Koma ine ndasankha kusangalala
[03:54.90] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[03:58.14] Koma ine ndasankha kusangalala
[04:03.48] Zokhumudwitsa ndi zambiri
[04:06.94] Koma ine ndasankha kusangalala
[04:12.00] Kusangalala, kusangalala
[04:20.58] Kusangalala, kusangalala
[04:33.62] Kusangalala, kusangalala
