Tempolale
[00:05.65] ...
[00:17.08] Baby don't worry
[00:20.80] usamaa dandaule
[00:25.58] usamaa kayikile
[00:28.78] masikuwa uzilemba mu daily
[00:34.63] mavutowa ndi history
[00:39.40] zonsezi nzakale kale
[00:43.38] chonde usazayiwaale
[00:47.10] masikuwa uzilemba mu daily
[00:52.95] zonsezi nzatempolale
[00:58.52] tempolale tempolale
[01:05.71] matsikuwa uzilemba mu daily
[01:11.55] zonsezi nzatempolale
[01:15.56] mavuto anthuwa nga tempolale
[01:20.07] misozi yathuyi tempolale
[01:24.32] masikuwa uzilemba mu daily
[01:30.16] koopya tadusa kale
[01:32.82] My lover
[01:34.15] zachuma tamukumbukile yobuu my lover
[01:38.66] za mwana tamukumbukile Salah my..
[01:42.91] amalanda amapatsa osayiwala
[01:46.36] my lover
[01:47.70] taona zambiri kufika lelo my lover
[01:53.55] nde ulova nkachani my lover
[01:57.54] Kusowa ya rent nkachani my lover
[02:02.32] kusowa ma fees nkachani my lover
[02:06.85] zonsezi ndiza tempolale
[02:11.10] mavuto anthuwa nga tempolale
[02:15.62] misonzi yathu nja tempolale
[02:19.60] masikuwa uzilemba mu daily
[02:25.44] zonsezi nzatempolale
[02:29.71] mavuto anthuwa nga tempolale
[02:33.96] misozi yathu nja tempolale
[02:37.94] masikuwa uzilemba mu daily
[02:45.52] olo mdima uwopse bwanji
[02:47.93] kunja kucha
[02:50.33] Namodwe awombe bwanji tiza woloka
[02:55.11] iwe ndi ineeee eeeeeh
[03:04.14] olo mdima uwopse bwanji
[03:06.54] kunja kucha
[03:08.93] namodwe awombe bwanji tiza woloka
[03:13.18] iwe ndi ineeee eeeh eeeh
[03:17.96] iwe ndi ineeee eeeh eeeh
[03:20.88] zonsezi ndiza tempolale
[03:26.47] tempolale tempolale
[03:31.00] masikuwa uzilemba mu daily
[03:39.23] zonsezi ndiza tempolale
[03:44.00] mavuto anthuwa nga tempolale
[03:48.00] misonzi yathu ija tempolale
[03:51.99] matsikuwa uzilemba mu daily
